2 MBIRI
ZIMENE ZILI MʼBUKULI
1
2
3
4
Guwa lansembe, thanki yosungira madzi ndi mabeseni (1-6)
Zoikapo nyale, matebulo ndi mabwalo (7-11a)
Kumaliza ntchito yomanga kachisi (11b-22)
5
6
7
Kachisi anadzazidwa ndi ulemerero wa Yehova (1-3)
Zikondwerero zotsegulira kachisi (4-10)
Yehova anaonekera kwa Solomo (11-22)
8
9
10
11
Ulamuliro wa Rehobowamu (1-12)
Alevi okhulupirika anasamukira ku Yuda (13-17)
Banja la Rehobowamu (18-23)
12
13
14
15
16
17
Yehosafati, mfumu ya Yuda (1-6)
Ntchito yophunzitsa anthu (7-9)
Asilikali amphamvu a Yehosafati (10-19)
18
Mgwirizano wa Yehosafati ndi Ahabu (1-11)
Mikaya analosera zoti agonjetsedwa (12-27)
Ahabu anaphedwa ku Ramoti-giliyadi (28-34)
19
20
Mayiko ozungulira anayamba kuopseza Ayuda (1-4)
Yehosafati anapempha Mulungu kuti amuthandize (5-13)
Mmene Yehova anamuyankhira (14-19)
Ayuda anapulumutsidwa modabwitsa (20-30)
Kutha kwa ulamuliro wa Yehosafati (31-37)
21
Yehoramu, mfumu ya Yuda (1-11)
Uthenga umene Eliya analemba (12-15)
Mapeto omvetsa chisoni a Yehoramu (16-20)
22
23
Yehoyada anathandiza kuti Yehoasi akhale mfumu (1-11)
Ataliya anaphedwa (12-15)
Zinthu zomwe Yehoyada anasintha (16-21)
24
Ulamuliro wa Yehoasi (1-3)
Yehoasi anakonza kachisi (4-14)
Yehoasi anayamba kulambira mafano (15-22)
Yehoasi anaphedwa (23-27)
25
Amaziya, mfumu ya Yuda (1-4)
Anamenyana ndi Aedomu (5-13)
Amaziya anayamba kulambira mafano (14-16)
Anamenyana ndi Yehoasi mfumu ya Isiraeli (17-24)
Imfa ya Amaziya (25-28)
26
Uziya, mfumu ya Yuda (1-5)
Nkhondo zimene Uziya anamenya (6-15)
Uziya anachititsidwa khate chifukwa chodzikuza (16-21)
Imfa ya Uziya (22, 23)
27
28
Ahazi, mfumu ya Yuda (1-4)
Anagonjetsedwa ndi Siriya komanso Isiraeli (5-8)
Odedi anachenjeza Isiraeli (9-15)
Ayuda anatsitsidwa (16-19)
Ahazi anayamba kulambira mafano; imfa ya Ahazi (20-27)
29
Hezekiya, mfumu ya Yuda (1, 2)
Zinthu zimene Hezekiya anasintha (3-11)
Kuyeretsa kachisi (12-19)
Anayambiranso utumiki wapakachisi (20-36)
30
31
32
Senakeribu anaopseza Yerusalemu (1-8)
Senakeribu ananyoza Yehova (9-19)
Mngelo anapha asilikali a Asiriya (20-23)
Hezekiya anadwala kenako anadzikuza (24-26)
Zimene Hezekiya anachita; imfa ya Hezekiya (27-33)
33
Manase, mfumu ya Yuda (1-9)
Manase analapa machimo ake (10-17)
Imfa ya Manase (18-20)
Amoni, mfumu ya Yuda (21-25)
34
Yosiya, mfumu ya Yuda (1, 2)
Zinthu zomwe Yosiya anasintha (3-13)
Anapeza buku la Chilamulo (14-21)
Hulida analosera za tsoka (22-28)
Yosiya anawerengera anthu buku (29-33)
35
36
Yehoahazi, mfumu ya Yuda (1-3)
Yehoyakimu, mfumu ya Yuda (4-8)
Yehoyakini, mfumu ya Yuda (9, 10)
Zedekiya, mfumu ya Yuda (11-14)
Yerusalemu anawonongedwa (15-21)
Koresi analamula kuti kachisi amangidwenso (22, 23)