EZEKIELI
ZIMENE ZILI MʼBUKULI
-  1  
-  2  
-  3  
-  4  
-  5  
-  6  
-  7  - 
- Mapeto afika (1-27) - 
- Tsoka loti silinaonekepo (5) 
- Ndalama zidzatayidwa mʼmisewu (19) 
- Kachisi adzaipitsidwa (22) 
 
 
-  8  
-  9  
- 10  - 
- Anatenga moto kuchokera pakati pa mawilo (1-8) 
- Anafotokoza zokhudza akerubi komanso mawilo (9-17) 
- Ulemerero wa Yehova unachoka pakachisi (18-22) 
 
- 11  - 
- Anadzudzula akalonga oipa (1-13) 
- Lonjezo lakubwezeretsa (14-21) 
- Ulemerero wa Mulungu unachoka mu Yerusalemu (22, 23) 
- Ezekieli anabwerera ku Kasidi mʼmasomphenya (24, 25) 
 
- 12  
- 13  
- 14  
- 15  
- 16  
- 17  
- 18  
- 19  
- 20  - 
- Mbiri ya kupanduka kwa Isiraeli (1-32) 
- Aisiraeli analonjezedwa kuti adzabwerera kwawo (33-44) 
- Ulosi wokhudza mbali yakumʼmwera (45-49) 
 
- 21  - 
- Mulungu adzasolola lupanga lake lachiweruzo (1-17) 
- Mfumu ya Babulo idzaukira Yerusalemu (18-24) 
- Mtsogoleri woipa wa Isiraeli adzachotsedwa pa udindo (25-27) 
- Lupanga lidzapha mbadwa za Amoni (28-32) 
 
- 22  - 
- Yerusalemu, mzinda wa mlandu wokhetsa magazi (1-16) 
- Isiraeli ali ngati zinthu zachabechabe zotsalira poyenga zitsulo (17-22) 
- Anadzudzula atsogoleri komanso anthu a mu Isiraeli (23-31) 
 
- 23  
- 24  
- 25  - 
- Ulosi wokhudza Amoni (1-7) 
- Ulosi wokhudza Mowabu (8-11) 
- Ulosi wokhudza Edomu (12-14) 
- Ulosi wokhudza Filisitiya (15-17) 
 
- 26  
- 27  
- 28  - 
- Ulosi wokhudza mfumu ya Turo (1-10) 
- Nyimbo yoimba polira yokhudza mfumu ya Turo (11-19) - 
- “Iwe unali mu Edeni” (13) 
- “Kerubi wodzozedwa amene amagwira ntchito yoteteza” (14) 
- “Unayamba kuchita zinthu zosalungama” (15) 
 
- Ulosi wokhudza Sidoni (20-24) 
- Isiraeli adzabwezeretsedwa mwakale (25, 26) 
 
- 29  
- 30  
- 31  
- 32  
- 33  - 
- Ntchito za mlonda (1-20) 
- Nkhani yokhudza kuwonongedwa kwa Yerusalemu (21, 22) 
- Uthenga wopita kwa anthu okhala mʼmabwinja a ku Yerusalemu (23-29) 
- Anthu atamva uthengawo, sanachite chilichonse (30-33) 
 
- 34  
- 35  
- 36  
- 37  
- 38  
- 39  - 
- Gogi ndi magulu ake a asilikali adzawonongedwa (1-10) 
- Adzaikidwa mʼmanda mʼChigwa cha Hamoni-Gogi (11-20) 
- Isiraeli adzabwereranso mwakale (21-29) 
 
- 40  - 
- Ezekieli anamupititsa ku Isiraeli mʼmasomphenya (1, 2) 
- Ezekieli anaona masomphenya a kachisi (3, 4) 
- Mabwalo ndi mageti (5-47) - 
- Geti lakunja lakumʼmawa (6-16) 
- Bwalo lakunja; mageti ena (17-26) 
- Bwalo lamkati ndi mageti (27-37) 
- Zipinda zochitiramo utumiki wapakachisi (38-46) 
- Guwa lansembe (47) 
 
- Khonde la kachisi (48, 49) 
 
- 41  - 
- Malo opatulika amʼkachisi (1-4) 
- Khoma komanso zipinda zamʼmbali (5-11) 
- Nyumba imene inali kumadzulo (12) 
- Anayeza nyumba zonse (13-15a) 
- Mkati mwa kachisi (15b-26) 
 
- 42  
- 43  
- 44  - 
- Geti lakumʼmawa linkakhala lotseka (1-3) 
- Malangizo okhudza alendo (4-9) 
- Malangizo okhudza Alevi ndi ansembe (10-31) 
 
- 45  - 
- Chopereka chopatulika komanso mzinda (1-6) 
- Malo amene mtsogoleri ankalandira (7, 8) 
- Atsogoleri azichita zinthu moona mtima (9-12) 
- Zinthu zimene anthu ankapereka komanso zimene mtsogoleri ankayenera kuchita (13-25) 
 
- 46  - 
- Nsembe zoperekedwa pazochitika zapadera (1-15) 
- Cholowa chochokera pamalo a mtsogoleri (16-18) 
- Malo amene ankawiritsirapo nsembe (19-24) 
 
- 47  
- 48