MATEYU
ZIMENE ZILI MʼBUKULI
-  1  
-  2  - 
- Okhulupirira nyenyezi anapita kukamuona (1-12) 
- Anathawira ku Iguputo (13-15) 
- Herode anapha ana aamuna (16-18) 
- Anabwerera ku Nazareti (19-23) 
 
-  3  
-  4  - 
- Mdyerekezi anayesa Yesu (1-11) 
- Yesu anayamba kulalikira ku Galileya (12-17) 
- Anasankha ophunzira oyambirira (18-22) 
- Yesu ankalalikira, kuphunzitsa komanso kuchiritsa (23-25) 
 
-  5  - 
- ULALIKI WAPAPHIRI (1-48) - 
- Yesu anayamba kuphunzitsa paphiri (1, 2) 
- Zinthu 9 zimene zimapangitsa anthu kuti azikhala osangalala (3-12) 
- Mchere komanso kuwala (13-16) 
- Yesu anakwaniritsa Chilamulo (17-20) 
- Malangizo okhudza mkwiyo (21-26), chigololo (27-30), kutha kwa ukwati (31, 32), malumbiro (33-37), kubwezera (38-42), kukonda adani athu (43-48) 
 
 
-  6  - 
- ULALIKI WAPAPHIRI (1-34) - 
- Muzipewa kudzionetsera kuti ndinu olungama (1-4) 
- Mmene tingapempherere (5-15) 
- Kusala kudya (16-18) 
- Chuma padziko lapansi komanso kumwamba (19-24) 
- Siyani kuda nkhawa (25-34) 
 
 
-  7  
-  8  - 
- Anachiritsa munthu wakhate (1-4) 
- Chikhulupiriro cha mtsogoleri wa asilikali (5-13) 
- Yesu anachiritsa anthu ambiri ku Kaperenao (14-17) 
- Zimene tingachite kuti tizitsatira Yesu (18-22) 
- Yesu analetsa mphepo yamphamvu (23-27) 
- Yesu anatumiza ziwanda munkhumba (28-34) 
 
-  9  - 
- Yesu anachiritsa munthu wakufa ziwalo (1-8) 
- Yesu anaitana Mateyu (9-13) 
- Funso lokhudza kusala kudya (14-17) 
- Mwana wamkazi wa Yairo; mzimayi anagwira chovala chakunja cha Yesu (18-26) 
- Yesu anachiritsa munthu wosaona komanso wosalankhula (27-34) 
- Zokolola nʼzochuluka, koma antchito ndi ochepa (35-38) 
 
- 10  - 
- Atumwi 12 (1-4) 
- Malangizo okhudza kulalikira (5-15) 
- Ophunzira adzazunzidwa (16-25) 
- Muziopa Mulungu, osati anthu (26-31) 
- Osati mtendere, koma lupanga (32-39) 
- Kulandira ophunzira a Yesu (40-42) 
 
- 11  - 
- Yohane Mʼbatizi analemekezedwa (1-15) 
- Anadzudzula mʼbadwo wosamvera (16-24) 
- Yesu anatamanda Atate wake chifukwa chokomera mtima anthu wamba (25-27) 
- Goli la Yesu limatsitsimula (28-30) 
 
- 12  - 
- Yesu ndi “Mbuye wa Sabata” (1-8) 
- Anachiritsa munthu wolumala dzanja (9-14) 
- Mtumiki amene Mulungu amamukonda (15-21) 
- Anatulutsa ziwanda pogwiritsa ntchito mzimu woyera (22-30) 
- Tchimo losakhululukidwa (31, 32) 
- Mtengo umadziwika ndi zipatso zake (33-37) 
- Chizindikiro cha Yona (38-42) 
- Mzimu wonyansa ukabwerera (43-45) 
- Amayi ake a Yesu komanso azichimwene ake (46-50) 
 
- 13  
- 14  - 
- Yohane Mʼbatizi anadulidwa mutu (1-12) 
- Yesu anadyetsa anthu 5,000 (13-21) 
- Yesu anayenda pamadzi (22-33) 
- Anachiritsa anthu ku Genesareti (34-36) 
 
- 15  - 
- Anadzudzula miyambo ya makolo (1-9) 
- Zodetsa zimachokera mumtima (10-20) 
- Chikhulupiriro cholimba cha mayi wa ku Foinike (21-28) 
- Yesu anachiritsa matenda ambiri (29-31) 
- Yesu anadyetsa anthu 4,000 (32-39) 
 
- 16  - 
- Kupempha chizindikiro (1-4) 
- Zofufumitsa za Afarisi ndi Asaduki (5-12) 
- Makiyi a Ufumu (13-20) 
- Ananeneratu zokhudza imfa ya Yesu (21-23) 
- Chizindikiro cha ophunzira enieni (24-28) 
 
- 17  - 
- Yesu anasintha maonekedwe (1-13) 
- Chikhulupiriro chofanana ndi kanjere ka mpiru (14-21) 
- Yesu ananeneratunso zokhudza imfa yake (22, 23) 
- Anapereka msonkho pogwiritsa ntchito ndalama yamkamwa mwa nsomba (24-27) 
 
- 18  - 
- Wamkulu kwambiri mu Ufumu (1-6) 
- Zopunthwitsa (7-11) 
- Fanizo la nkhosa yosochera (12-14) 
- Zimene tingachite kuti tibweze mʼbale wathu (15-20) 
- Fanizo la kapolo wosakhululuka (21-35) 
 
- 19  - 
- Ukwati komanso kutha kwa banja (1-9) 
- Mphatso ya kusakwatira (10-12) 
- Yesu anadalitsa ana (13-15) 
- Funso limene wachinyamata wolemera anafunsa (16-24) 
- Zinthu zimene tiyenera kudzimana chifukwa cha Ufumu (25-30) 
 
- 20  - 
- Anthu amene ankagwira ntchito mʼmunda wampesa analandira malipiro ofanana (1-16) 
- Yesu ananeneratunso zokhudza imfa yake (17-19) 
- Anapempha kuti adzapatsidwe malo apadera mu Ufumu (20-28) 
- Amuna awiri osaona anachiritsidwa (29-34) 
 
- 21  - 
- Yesu analowa mumzinda mwaulemerero (1-11) 
- Yesu anayeretsa kachisi (12-17) 
- Anatemberera mtengo wa mkuyu (18-22) 
- Anakayikira ulamuliro wa Yesu (23-27) 
- Fanizo la ana awiri aamuna (28-32) 
- Fanizo la alimi amene anapha anthu (33-46) 
 
- 22  - 
- Fanizo la phwando laukwati (1-14) 
- Mulungu komanso Kaisara (15-22) 
- Funso lokhudza kuukitsidwa kwa akufa (23-33) 
- Malamulo awiri akuluakulu (34-40) 
- Kodi Khristu ndi mwana wa Davide? (41-46) 
 
- 23  - 
- Musamatsanzire alembi ndi Afarisi (1-12) 
- Tsoka kwa alembi ndi Afarisi (13-36) 
- Yesu analirira Yerusalemu (37-39) 
 
- 24  
- 25  
- 26  - 
- Ansembe anakonza chiwembu kuti aphe Yesu (1-5) 
- Yesu anathiridwa mafuta onunkhira (6-13) 
- Pasika womaliza komanso kuperekedwa (14-25) 
- Anayambitsa mwambo wa Chakudya Chamadzulo cha Ambuye (26-30) 
- Ananeneratu kuti Petulo adzamukana (31-35) 
- Yesu anapemphera ku Getsemane (36-46) 
- Yesu anagwidwa (47-56) 
- Anazengedwa mlandu ndi Khoti Lalikulu la Ayuda (57-68) 
- Petulo anakana Yesu (69-75) 
 
- 27  - 
- Yesu anaperekedwa kwa Pilato (1, 2) 
- Yudasi anadzimangirira (3-10) 
- Yesu anaonekera kwa Pilato (11-26) 
- Anamuchitira zachipongwe pamaso pa anthu (27-31) 
- Anamukhomerera pamtengo ku Gologota (32-44) 
- Imfa ya Yesu (45-56) 
- Kuikidwa mʼmanda kwa Yesu (57-61) 
- Anakhwimitsa chitetezo pamanda ake (62-66) 
 
- 28