NYIMBO 118
“Tiwonjezereni Chikhulupiriro”
zosindikizidwa
	- 1. Yehova ndifedi anthu ochimwa, - Zoipa zimadzadza mumtima. - Pali tchimo lomwe limatikola— - Kusowa kwa chikhulupiriro. - (KOLASI) - M’tionjezere chikhulupiriro. - Tikupempha kwa inu Yehova. - Mwa chifundo chanu m’tionjezere, - Tikulemekezeni mu zonse. 
- 2. N’zosatheka kukusangalatsani. - Ngati sitimakhulupirira. - Chikhulupiriro chimateteza. - Ndipo chimatilimbitsa mtima. - (KOLASI) - M’tionjezere chikhulupiriro. - Tikupempha kwa inu Yehova. - Mwa chifundo chanu m’tionjezere, - Tikulemekezeni mu zonse. 
(Onaninso Gen. 8:21; Aheb. 11:6; 12:1.)