‘Imvani Zimene Mzimu Ukunena ku Mipingo’
M’mawa
9:40 Kumvetsera Nyimbo
9:50 Nyimbo Na. 1 ndi Pemphero
10:00 Kodi Tingamve Bwanji “Zimene Mzimu Ukunena?”
10:15 “Sunafooke”
10:30 “Usachite Mantha”
10:55 Nyimbo Na. 73 ndi Zilengezo
11:05 “Sunakane Kuti Umandikhulupirira”
11:35 Nkhani ya Ubatizo: N’chifukwa Chiyani Mukubatizidwa?
12:05 Nyimbo Na. 79
Masana
1:20 Kumvetsera Nyimbo
1:30 Nyimbo Na. 126
1:35 Zochitika pa Moyo wa Chikhristu
1:45 Phunziro Lachidule la Nsanja ya Olonda
2:15 Nkhani Yosiyirana: Mmene Tingagwiritsire Ntchito Malangizo
• “Gwirani Mwamphamvu Zinthu Zabwino Zimene Muli Nazo”
• ‘Khala Maso, Ndipo Khala Olimba’
• “Ndatsegula Khomo Pamaso Pako”
3:00 Nyimbo Na. 76 ndi Zilengezo
3:10 ‘Khalani Odzipereka’
3:55 Nyimbo Na. 129 ndi Pemphero