‘Muzilambira Motsogoleredwa Ndi Mzimu Komanso Choonadi’
M’mawa
9:40 Kumvetsera Nyimbo
9:50 Nyimbo Na. 85 ndi Pemphero
10:00 “Atate Akufuna Anthu Ngati Amenewo”
10:15 Nkhani Yosiyirana: ‘Muzilambira Motsogoleredwa Ndi Mzimu’
• Mukamayesetsa Kuti Mumvetse Malangizo a Yehova
• Mukakhumudwa
• Mukamafuna Kuti Muzichita Zambiri Potumikira Yehova
11:05 Nyimbo Na. 88 ndi Zilengezo
11:15 Kodi ‘Timachititsa Bwanji Choonadi Kuti Chidziwike’?
11:35 Nkhani ya Ubatizo: N’chifukwa Chiyani Mukubatizidwa?
12:05 Nyimbo Na. 51
Masana
1:20 Kumvetsera Nyimbo
1:30 Nyimbo Na. 72 ndi Pemphero
1:35 Nkhani ya Onse: Kodi Tingadziwe Bwanji Zoyenera ndi Zosayenera?
2:05 Phunziro Lachidule la Nsanja ya Olonda
2:35 Nyimbo Na. 56 ndi Zilengezo
2:45 Nkhani Yosiyirana: ‘Muzilambira Motsogoleredwa Ndi Choonadi’
• M’banja
• M’dziko Logawanikali
• Mukakhala pa Mavuto Azachuma
3:30 “Gula Choonadi Ndipo Usachigulitse”
4:00 Nyimbo Na. 29 ndi Pemphero