Mawu a M'munsi “Mankhusu” ndi makoko amene amachotsa kumbewu ngati mpunga popuntha ndipo amatha kuwauluza ndi mphepo.