Mawu a M'munsi
a Zikuoneka kuti mzinda wa Samariya, womwe unali likulu la dziko la Isiraeli, unali ndi anthu 20,000 kapena 30,000 m’nthawi ya Yona. Koma chiwerengerochi chinali chochepa kwambiri poyerekeza ndi chiwerengero cha anthu a ku Nineve. Pa nthawi imene mzinda wa Nineve unali wotukuka kwambiri, uyenera kuti unali waukulu kwambiri padziko lonse.