Mawu a M'munsi
c Ponena kuti anthuwo sankadziwa kusiyanitsa dzanja lawo lamanja ndi lamanzere, Mulungu ankatanthauza kuti iwo anali ngati ana ndipo sankadziwa chilichonse chokhudza malamulo ake.