Mawu a M'munsi
a M’Baibulo muli nkhani zinanso za anthu amene anaukitsidwa. Anthu amenewa anali ana, akuluakulu, amuna, akazi, Aisiraeli komanso anthu amitundu ina. Mukhoza kuwerenga nkhani zimenezi pa 1 Mafumu 17:17-24; 2 Mafumu 4:32-37; 13:20, 21; Mateyu 28:5-7; Luka 7:11-17; 8:40-56; Machitidwe 9:36-42; 20:7-12.