Mawu a M'munsi
b MATANTHAUZO A MAWU ENA: Kufatsa. Anthu ofatsa amakhala odekha pochita zinthu ndi anzawo ndipo sapsa mtima ngakhale ataputidwa. Kudzichepetsa. Anthu odzichepetsa sadzikuza kapena kudzitama ndipo amaona kuti anthu ena ndi owaposa. Yehova ndi wodzichepetsanso chifukwa ngakhale kuti ndi wamkulu kwambiri amachita zinthu ndi ena mwachikondi komanso mwachifundo.