Mawu a M'munsi
e MAWU OFOTOKOZERA CHITHUNZI: Akhristu amene ali m’ndende chifukwa chotsatira zimene amakhulupirira komanso amene amalalikira ndi kuphunzitsa anthu mwaufulu, amayembekezera kudzakhala padziko lapansi Ufumu wa Mulungu ukamadzalamulira.