Mawu a M'munsi b Kuti mudziwe zambiri, onani mutu 9 wa buku lakuti, Baibulo—Kodi Ndilo Mawu a Mulungu Kapena a Munthu? lofalitsidwa ndi Mboni za Yehova. Bukuli likupezeka pawebusaiti yathu ya www.pr2711.com pamene alemba kuti LAIBULALE > MABUKU.