Mawu a M'munsi
b Mungapezenso nkhani zokhudza zochitika pa moyo wa anthu ena (1) mu Buku la Mboni za Yehova Lofufuzira Nkhani pa mutu wakuti “Baibulo,” “Lothandiza,” kenako “‘Baibulo Limasintha Anthu” (Nkhani za mu Nsanja ya Olonda)” komanso (2) pa JW Library® pa gawo la “Media,” pachigawo chakuti “Zochitika pa Moyo wa Anthu Ena.”