Mawu a M'munsi
a Yehova amafunitsitsa kukhululukira anthu ochimwa omwe alapa. Monga Akhristu, timafunika kutengera chitsanzo chake ena akatilakwira. Munkhaniyi tikambirana machimo omwe tikhoza kungokhululuka patokha komanso machimo amene tiyenera kudziwitsa akulu. Tionanso chifukwa chake Yehova amafuna kuti tizikhululukirana komanso madalitso omwe timapeza tikamachita zimenezi.