Mawu a M'munsi
a Kwa ambiri, kupeza chimwemwe chenicheni n’kovuta chifukwa amachifunafuna m’njira yolakwika pochita zosangalatsa, kufunafuna chuma, kutchuka kapena udindo. Koma Yesu ali padzikoli anauza anthu zimene angachite kuti apeze chimwemwe chenicheni. Munkhaniyi tikambirana zinthu zitatu zomwe zingatithandize kuti tipeze chimwemwe chenicheni.