NYIMBO 147
Mulungu Watilonjeza Moyo Wosatha
zosindikizidwa
	- 1. Mulungu watilonjeza. - Moyo womwe sudzatha. - ‘Ofatsa ’dzasangalala.’ - Zidzachitikadi. - (KOLASI) - Tidzakhala ndithu, - Ndi moyo wosatha. - M’lungu walonjeza. - Zidzachitika. 
- 2. Paradaiso akubwera; - Anthu adzamasuka. - Kudzakhaladi mtendere, - Wochoka kwa M’lungu. - (KOLASI) - Tidzakhala ndithu, - Ndi moyo wosatha. - M’lungu walonjeza. - Zidzachitika. 
- 3. Akufawo adzauka, - Chisoninso chidzatha. - Mulungu adzapukuta, - Misozi ya anthu. - (KOLASI) - Tidzakhala ndithu, - Ndi moyo wosatha. - M’lungu walonjeza. - Zidzachitika. 
(Onaninso Yes. 25:8; Luka 23:43; Yoh. 11:25; Chiv. 21:4.)