NYIMBO 60
Akamvera Adzapeza Moyo
zosindikizidwa
	- 1. Mulungu akufuna - tichenjeze anthu - Kuti tsiku la mkwiyo - wake likubwera. - (KOLASI) - Akamvera adzapeza, - Inde moyo wosatha. - Nafe tidzapulumuka, - Tikafalitsa uthenga, - Uthenga. 
- 2. Tili ndi uthenga - woti tiuze anthu. - Tiitane anthu abwere - kwa Mulungu. - (KOLASI) - Akamvera adzapeza, - Inde moyo wosatha. - Nafe tidzapulumuka, - Tikafalitsa uthenga, - Uthenga. - (VESI LOKOMETSERA) - Mwamsanga tilengeze, - Anthu amve, aphunzire. - Cho’nadi tiphunzitse, - Kuti moyo adzapeze. - (KOLASI) - Akamvera adzapeza, - Inde moyo wosatha. - Nafe tidzapulumuka, - Tikafalitsa uthenga, - Uthenga. 
(Onaninso 2 Mbiri 36:15; Yes. 61:2; Ezek. 33:6; 2 Ates. 1:8.)