1 MBIRI
ZIMENE ZILI MʼBUKULI
-  1  - 
- Kuchokera pa Adamu kufika pa Abulahamu (1-27) 
- Mbadwa za Abulahamu (28-37) 
- Aedomu ndi mafumu awo (38-54) 
 
-  2  - 
- Ana 12 a Isiraeli (1, 2) 
- Mbadwa za Yuda (3-55) 
 
-  3  
-  4  
-  5  
-  6  
-  7  - 
- Mbadwa za Isakara (1-5), za Benjamini (6-12), za Nafitali (13), za Manase (14-19), za Efuraimu (20-29), ndi za Aseri (30-40) 
 
-  8  
-  9  
- 10  
- 11  - 
- Aisiraeli onse anadzoza Davide kukhala mfumu (1-3) 
- Davide analanda mzinda wa Ziyoni (4-9) 
- Asilikali amphamvu a Davide (10-47) 
 
- 12  
- 13  
- 14  
- 15  
- 16  - 
- Likasa linaikidwa mutenti (1-6) 
- Nyimbo ya Davide yothokoza (7-36) 
- Utumiki wa kumene kunali Likasa (37-43) 
 
- 17  - 
- Davide anauzidwa kuti sadzamanga kachisi (1-6) 
- Pangano la ufumu ndi Davide (7-15) 
- Pemphero la Davide loyamika (16-27) 
 
- 18  
- 19  
- 20  
- 21  - 
- Davide anawerenga anthu mosavomerezeka (1-6) 
- Chilango chochokera kwa Yehova (7-17) 
- Davide anamanga guwa (18-30) 
 
- 22  - 
- Davide anakonzekera zinthu zomangira kachisi (1-5) 
- Davide anapereka malangizo kwa Solomo (6-16) 
- Akalonga analamulidwa kuti athandize Solomo (17-19) 
 
- 23  
- 24  
- 25  
- 26  
- 27  
- 28  
- 29  - 
- Zopereka zothandiza pomanga kachisi (1-9) 
- Pemphero la Davide (10-19) 
- Anthu anasangalala; ufumu wa Solomo (20-25) 
- Imfa ya Davide (26-30)