NUMERI
ZIMENE ZILI MʼBUKULI
1
Kalembera wa amuna oyenera kupita kunkhondo (1-46)
Alevi sankayenera kupita nawo kunkhondo (47-51)
Dongosolo lomangira matenti mumsasa (52-54)
2
3
4
Utumiki wa Akohati (1-20)
Utumiki wa Agerisoni (21-28)
Utumiki wa Amerari (29-33)
Mmene kalembera anayendera (34-49)
5
Kuika munthu wodetsedwa kwayekha (1-4)
Kuulula tchimo komanso kulipira (5-10)
Kumwetsa madzi munthu amene akumuganizira kuti wachita chigololo (11-31)
6
7
8
Aroni anayatsa nyale 7 (1-4)
Alevi anayeretsedwa nʼkuyamba kutumikira (5-22)
Zaka zimene Alevi ankayenera kuyamba komanso kusiya utumiki (23-26)
9
10
Malipenga asiliva (1-10)
Anachoka ku Sinai (11-13)
Dongosolo la kayendedwe (14-28)
Hobabu anapemphedwa kuti alondolere njira Aisiraeli (29-34)
Pemphero limene Mose anapereka ponyamuka (35, 36)
11
Mulungu anawabweretsera moto chifukwa chodandaula (1-3)
Anthu anayamba kulirira nyama (4-9)
Mose ankadziona kuti ndi wosayenerera (10-15)
Yehova anapereka mzimu kwa akulu 70 (16-25)
Eledadi ndi Medadi; Yoswa anachita nsanje chifukwa choti ankadera nkhawa Mose (26-30)
Anabweretsa zinziri; anthu analangidwa chifukwa cha dyera (31-35)
12
Miriamu ndi Aroni anakangana ndi Mose (1-3)
Yehova anaikira kumbuyo Mose (4-8)
Miriamu anachita khate (9-16)
13
14
Anthu ankafuna kubwerera ku Iguputo (1-10)
Yehova anakwiya; Mose anapepesa (11-19)
Chilango: zaka 40 mʼchipululu (20-38)
Aisiraeli anagonjetsedwa ndi Aamaleki (39-45)
15
Malamulo okhudza nsembe (1-21)
Nsembe za machimo amene munthu wachita mosadziwa (22-29)
Chilango cha munthu amene wachimwa mwadala (30, 31)
Munthu amene anaphwanya Sabata anamupha (32-36)
Zovala zizikhala ndi ulusi mʼmphepete (37-41)
16
17
18
Ntchito za ansembe ndi Alevi (1-7)
Gawo limene ansembe ankalandira (8-19)
Alevi azilandira komanso kupereka chakhumi (20-32)
19
20
Miriamu anamwalira ku Kadesi (1)
Mose anamenya thanthwe nʼkuchimwa (2-13)
Aedomu anakana kuti Aisiraeli adutse mʼdziko lawo (14-21)
Imfa ya Aroni (22-29)
21
Mfumu ya ku Aradi inagonjetsedwa (1-3)
Njoka yakopa (4-9)
Aisiraeli anayenda mozungulira Mowabu (10-20)
Sihoni Mfumu ya Aamori inagonjetsedwa (21-30)
Ogi Mfumu ya Aamori inagonjetsedwa (31-35)
22
23
24
25
26
27
28
29
30
31
32
33
34
35
36