B14-A
Miyezo ya Zinthu Ndiponso Malonda
- Miyezo ya Zinthu Zamadzi 
- Kori (Mitsuko 10 / Mahini 60) - Malita 220 / Magaloni 58.1 
- Mtsuko (Mahini 6) - Malita 22 / Magaloni 5.81 
- Hini (Malogi 12) - Malita 3.67 / Mapainti 7.75 
- Logi (1⁄12 hini) - Malita 0.31 / Mapainti 0.66 
- Miyezo ya Zinthu Zomwe Si Zamadzi 
- Homeri (Kori imodzi / Maefa 10) - Malita 220 
- Efa (Maseya atatu / Maomeri 10) - Malita 22 
- Seya (Maomeri 31⁄3) - Malita 7.33 
- Omeri (Makabu 14⁄5) - Malita 2.2 / Makwati 2 
- Kabu - Malita 1.22 / Makwati 1.11 
- Kwati - Malita 1.08 
- Miyezo Yoyezera Mtunda 
- Bango lalitali (Mikono 6 yaitali) - Mamita 3.11 / Mafiti 10.2 
- Bango (Mikono 6) - Mamita 2.67 / Mafiti 8.75 
- Fatomu - Mamita 1.8 / Mafiti 6 
- Mkono umodzi (Zikhatho 7) - Masentimita 51.8 / Mainchesi 20.4 
- Mkono (Masipani awiri / Zikhatho 6) - Masentimita 44.5 / Mainchesi 17.5 
- Mkono waufupi - Masentimita 38 / Mainchesi 15 
- Sitadiya imodzi ya Chiroma 1⁄8 ya mailo ya Chiroma - = Mamita 185 / Mafiti 606.95 
- 1 Mphipi imodzi ya chala (1⁄4 ya chikhatho) - Masentimita 1.85 / Mainchesi 0.73 
- 2 Chikhatho (Mphipi ya zala 4) - Masentimita 7.4 / Mainchesi 2.9 
- 3 Sipani (Zikhatho zitatu) - Masentimita 22.2 / Mainchesi 8.75