B14-B
Ndalama ndi Kulemera
Ndalama ndi Kulemera kwa Zinthu MʼMalemba a Chiheberi
| Gera (1⁄20 ya sekeli) Magalamu 0.57 Magera 10 = Beka imodzi | 
| Beka Magalamu 5.7 Mabeka awiri = Sekeli imodzi | 
| Pimu Magalamu 7.8 Pimu imodzi = 2⁄3 ya sekeli | 
| Kulemera kwa sekeli Sekeli Magalamu 11.4 Masekeli 50 = Mina imodzi | 
| Mina Magalamu 570 Ma mina 60 = Talente imodzi | 
| Talente Makilogalamu 34.2 | 
| Dariki (ya ku Perisiya, yagolide) Magalamu 8.4 | 
Ndalama ndi Kulemera kwa Zinthu MʼMalemba a Chigiriki
| Leputoni (ya Ayuda, yamkuwa) 1⁄2 ya kwadiransi | 
| Kwadiransi (ya Aroma, yamkuwa) Maleputa awiri | 
| Asariyoni (ya Aroma ndi madera ozungulira, yamkuwa) Makwadiransi 4 | 
| Dinari (ya Aroma, yasiliva) Makwadiransi 64 Magalamu 3.85 Malipiro a Tsiku Limodzi (Maola 12) Malipiro a Masiku Awiri | 
| Dalakima (ya Agiriki, yasiliva) Magalamu 3.4 Malipiro a Tsiku Limodzi (Maola 12) | 
| Didalakima (ya Agiriki, yasiliva) Madalakima awiri Magalamu 6.8 Malipiro a Masiku Atatu | 
| Tetiradalakima ya ku Antiokeya Tetiradalakima ya ku Turo (Sekeli yasiliva ya ku Turo) Tetiradalakima (ya Agiriki, yasiliva; imatchedwanso siteta yasiliva) Madalakima 4 Magalamu 13.6 Malipiro a Masiku 4 | 
| Mina Madalakima 100 Magalamu 340 = Malipiro a masiku pafupifupi 100 | 
| Talente Ma mina 60 Makilogalamu 20.4 = Malipiro a zaka pafupifupi 20 | 
| Paundi (ya Aroma) Magalamu 327 
 |