Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Chivumbulutso 15
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

Chivumbulutso 15:1

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 1:1
  • +Chv 16:1
  • +Le 26:21
  • +Chv 16:17
  • +Sl 7:11

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 215-216

Chivumbulutso 15:2

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +1Mf 7:23, 39
  • +Chv 2:7
  • +Chv 13:15
  • +Chv 13:18
  • +Chv 4:6
  • +Chv 5:8

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 216-217

Chivumbulutso 15:3

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eks 15:1; De 31:30; Ahe 3:5
  • +Yoh 1:29; Mac 3:22; Ahe 2:12
  • +Eks 15:11; Sl 92:5; 111:2; 139:14
  • +Eks 6:3; Chv 19:6
  • +De 32:4; Sl 145:17
  • +Yer 10:10; 1Ti 1:17

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,

    Yandikirani, tsa. 12

    Zimene Baibulo Limaphunzitsa, ptsa. 13-14

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 217-218

    Nsanja ya Olonda,

    4/1/1996, ptsa. 14-15

Chivumbulutso 15:4

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Yer 10:7
  • +Sl 22:23; 33:8
  • +Sl 86:12; Yoh 12:28
  • +Yer 3:12
  • +Sl 86:9; Mki 1:11
  • +Yes 2:4

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Yandikirani, ptsa. 282-283

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 217-218

    Nsanja ya Olonda,

    4/1/1996, ptsa. 14-15

    1/1/1992, ptsa. 18-19

Chivumbulutso 15:5

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Ahe 8:2; 9:11
  • +Mac 7:44
  • +Chv 11:19

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 218

Chivumbulutso 15:6

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 8:2
  • +Chv 15:1
  • +Da 10:5

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 218-219

Chivumbulutso 15:7

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Chv 19:4
  • +Sl 75:8; Yer 25:15; Chv 14:10
  • +Sl 90:2; 1Ti 1:17

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 218-219

Chivumbulutso 15:8

Malifalensi Opezeka Pakati pa Tsamba

  • +Eks 40:34; 1Mf 8:11; Yes 6:4; Eze 44:4
  • +Le 26:21; Chv 15:1

Kalozera

  • Buku Lofufuzira Nkhani

    Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 219-220

Mabaibulo Ena

Dinani pa nambala ya vesi kuti muone mavesi a m'Baibulo lina ofanana ndi vesilo.

Malemba Ena

Chiv. 15:1Chv 1:1
Chiv. 15:1Chv 16:1
Chiv. 15:1Le 26:21
Chiv. 15:1Chv 16:17
Chiv. 15:1Sl 7:11
Chiv. 15:21Mf 7:23, 39
Chiv. 15:2Chv 2:7
Chiv. 15:2Chv 13:15
Chiv. 15:2Chv 13:18
Chiv. 15:2Chv 4:6
Chiv. 15:2Chv 5:8
Chiv. 15:3Eks 15:1; De 31:30; Ahe 3:5
Chiv. 15:3Yoh 1:29; Mac 3:22; Ahe 2:12
Chiv. 15:3Eks 15:11; Sl 92:5; 111:2; 139:14
Chiv. 15:3Eks 6:3; Chv 19:6
Chiv. 15:3De 32:4; Sl 145:17
Chiv. 15:3Yer 10:10; 1Ti 1:17
Chiv. 15:4Yer 10:7
Chiv. 15:4Sl 22:23; 33:8
Chiv. 15:4Sl 86:12; Yoh 12:28
Chiv. 15:4Yer 3:12
Chiv. 15:4Sl 86:9; Mki 1:11
Chiv. 15:4Yes 2:4
Chiv. 15:5Ahe 8:2; 9:11
Chiv. 15:5Mac 7:44
Chiv. 15:5Chv 11:19
Chiv. 15:6Chv 8:2
Chiv. 15:6Chv 15:1
Chiv. 15:6Da 10:5
Chiv. 15:7Chv 19:4
Chiv. 15:7Sl 75:8; Yer 25:15; Chv 14:10
Chiv. 15:7Sl 90:2; 1Ti 1:17
Chiv. 15:8Eks 40:34; 1Mf 8:11; Yes 6:4; Eze 44:4
Chiv. 15:8Le 26:21; Chv 15:1
  • Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Werengani mu Baibulo la Dziko Latsopano (nwt)
  • 1
  • 2
  • 3
  • 4
  • 5
  • 6
  • 7
  • 8
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
Chivumbulutso 15:1-8

Chivumbulutso

15 Ndipo ndinaona chizindikiro china+ kumwamba, chachikulu ndi chodabwitsa. Ndicho angelo 7+ okhala ndi miliri 7.+ Imeneyi ndiyo yomaliza, chifukwa ndiyo ikumalizitsa+ mkwiyo+ wa Mulungu.

2 Kenako ndinaona chooneka ngati nyanja yagalasi+ yosakanikirana ndi moto. Ndipo amene anagonjetsa+ chilombo chija, chifaniziro chake,+ ndi nambala+ ya dzina lake, ndinawaona ataimirira pambali pa nyanja yagalasiyo,+ ali ndi azeze+ a Mulungu. 3 Iwo akuimba nyimbo ya Mose+ kapolo wa Mulungu, ndi nyimbo ya Mwanawankhosa,+ yakuti:

“Ntchito zanu n’zazikulu ndi zodabwitsa,+ inu Yehova Mulungu Wamphamvuyonse.+ Njira zanu ndi zolungama ndi zoona,+ inu Mfumu yamuyaya.+ 4 Kodi ndani sadzakuopani,+ inu Yehova?+ Ndani sadzalemekeza dzina lanu?+ Pakuti inu nokha ndinu wokhulupirika.+ Mitundu yonse ya anthu idzabwera kudzalambira pamaso panu,+ chifukwa malamulo anu olungama aonekera.”+

5 Zimenezi zitatha, ndinaona malo opatulika a m’chihema+ cha umboni+ atatsegulidwa kumwamba.+ 6 Ndipo angelo 7+ okhala ndi miliri 7+ aja anatuluka kumalo opatulikawo, atavala zovala zoyera+ ndi zowala, atavalanso zoteteza pachifuwa zagolide. 7 Ndiye chimodzi cha zamoyo zinayi+ zija chinapatsa angelo 7 amenewo mbale zagolide 7, zodzaza ndi mkwiyo wa Mulungu,+ amene adzakhala ndi moyo kwamuyaya.+ 8 Ndipo malo opatulikawo anadzaza utsi chifukwa cha ulemerero wa Mulungu,+ ndiponso chifukwa cha mphamvu zake. Palibe amene anatha kulowa m’malo opatulikawo, mpaka miliri 7+ ya angelo 7 aja itatha.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena