Genesis 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsopano m’dzikomo munagwa njala, ndipo Abulamu ananyamuka kulowera ku Iguputo kukakhala kumeneko monga mlendo.+ Anatero chifukwa njalayo inafika poipa kwambiri m’dzikomo.+
10 Tsopano m’dzikomo munagwa njala, ndipo Abulamu ananyamuka kulowera ku Iguputo kukakhala kumeneko monga mlendo.+ Anatero chifukwa njalayo inafika poipa kwambiri m’dzikomo.+