Genesis 12:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Odalitsa iwe ndidzawadalitsa, ndipo otemberera iwe ndidzawatemberera.+ Mabanja onse a padziko lapansi adzapeza madalitso* chifukwa cha iwe.”+ Genesis 22:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kudzera mwa mbewu yako,+ mitundu yonse ya padziko lapansi idzapeza madalitso* ndithu chifukwa chakuti wamvera mawu anga.’”+ Machitidwe 3:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Inu ndinu ana+ a aneneri ndi a pangano limene Mulungu anapangana ndi makolo anu akale. Iye anauza Abulahamu kuti, ‘Kudzera mwa mbewu yako mabanja onse a padziko lapansi adzadalitsidwa.’+ Agalatiya 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno, Malemba ataoneratu kuti Mulungu adzayesa anthu a mitundu ina kukhala olungama chifukwa cha chikhulupiriro, analengezeratu uthenga wabwino kwa Abulahamu, kuti: “Kudzera mwa iwe, mitundu yonse idzadalitsidwa.”+
3 Odalitsa iwe ndidzawadalitsa, ndipo otemberera iwe ndidzawatemberera.+ Mabanja onse a padziko lapansi adzapeza madalitso* chifukwa cha iwe.”+
18 Kudzera mwa mbewu yako,+ mitundu yonse ya padziko lapansi idzapeza madalitso* ndithu chifukwa chakuti wamvera mawu anga.’”+
25 Inu ndinu ana+ a aneneri ndi a pangano limene Mulungu anapangana ndi makolo anu akale. Iye anauza Abulahamu kuti, ‘Kudzera mwa mbewu yako mabanja onse a padziko lapansi adzadalitsidwa.’+
8 Ndiyeno, Malemba ataoneratu kuti Mulungu adzayesa anthu a mitundu ina kukhala olungama chifukwa cha chikhulupiriro, analengezeratu uthenga wabwino kwa Abulahamu, kuti: “Kudzera mwa iwe, mitundu yonse idzadalitsidwa.”+