Genesis 37:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Abale akewo anachita naye kaduka,+ koma bambo ake anasunga mawuwo.+ 1 Samueli 18:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kuyambira tsiku limenelo, Sauli anayamba kuyang’ana Davide ndi diso loipa.+ Miyambo 27:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mkwiyo umasefukira ndipo ukali ndi wankhanza,+ koma nsanje ndani angaipirire?+ Aroma 1:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 popeza anadzazidwa ndi zosalungama+ zonse, kuipa+ konse, kusirira konse kwa nsanje,+ ndi uchimo+ wonse. Mtima wawo unadzala kaduka,+ umbanda,+ ndewu,+ chinyengo+ ndi njiru.+ Anakonda manong’onong’o+ Tito 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti ngakhale ife nthawi inayake tinali opanda nzeru, osamvera, osocheretsedwa, akapolo a zilakolako ndi zosangalatsa zosiyanasiyana, ochita zoipa, akaduka, onyansa ndiponso achidani.+
29 popeza anadzazidwa ndi zosalungama+ zonse, kuipa+ konse, kusirira konse kwa nsanje,+ ndi uchimo+ wonse. Mtima wawo unadzala kaduka,+ umbanda,+ ndewu,+ chinyengo+ ndi njiru.+ Anakonda manong’onong’o+
3 Pakuti ngakhale ife nthawi inayake tinali opanda nzeru, osamvera, osocheretsedwa, akapolo a zilakolako ndi zosangalatsa zosiyanasiyana, ochita zoipa, akaduka, onyansa ndiponso achidani.+