Genesis 10:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Choncho malire a dziko la Akanani anachokera ku Sidoni mpaka ku Gerari+ kufupi ndi Gaza,+ n’kukafika ku Sodomu ndi Gomora+ mpakanso ku Adima+ ndi Zeboyimu,+ kufupi ndi Lasa. Genesis 20:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tsopano Abulahamu anasamutsa msasa wake+ n’kupita kudziko la Negebu. Kenako anakakhala monga mlendo ku Gerari+ pakati pa Kadesi+ ndi Shura.+
19 Choncho malire a dziko la Akanani anachokera ku Sidoni mpaka ku Gerari+ kufupi ndi Gaza,+ n’kukafika ku Sodomu ndi Gomora+ mpakanso ku Adima+ ndi Zeboyimu,+ kufupi ndi Lasa.
20 Tsopano Abulahamu anasamutsa msasa wake+ n’kupita kudziko la Negebu. Kenako anakakhala monga mlendo ku Gerari+ pakati pa Kadesi+ ndi Shura.+