Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 21:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Ndiyeno pa nthawi imeneyo, Abimeleki limodzi ndi Fikolo mkulu wa gulu lake lankhondo anauza Abulahamu kuti: “Mulungu ali ndi iwe pa zonse zomwe ukuchita.+

  • Genesis 39:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Kuyambira pamene Potifara anasankha Yosefe kukhala woyang’anira nyumba yake ndi zinthu zake zonse, Yehova anapitiriza kudalitsa nyumba ya Mwiguputoyo chifukwa cha Yosefe. Yehova anadalitsa zonse za m’nyumba ya Potifara ndi zakumunda zomwe.+

  • Yoswa 3:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ndipo Yehova anauza Yoswa kuti: “Lero ndiyamba kukukuza pamaso pa Aisiraeli onse,+ n’cholinga choti adziwe kuti monga mmene ndinakhalira ndi Mose,+ ndidzakhalanso ndi iwe.+

  • Zekariya 8:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 “Yehova wa makamu wanena kuti, ‘M’masiku amenewo, amuna 10 ochokera m’zilankhulo zonse za anthu a mitundu ina+ adzagwira+ chovala cha munthu amene ndi Myuda+ ndi kunena kuti: “Anthu inu tipita nanu limodzi,+ chifukwa tamva kuti Mulungu ali ndi inu.”’”+

  • 1 Akorinto 14:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Zobisika za mumtima mwake zimaululika,+ moti adzagwada n’kuwerama mpaka nkhope yake pansi, n’kulambira Mulungu, ndi kunena kuti: “Zoonadi Mulungu ali pakati panu.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena