Genesis 21:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ndiyeno Abulahamu anatenga nkhosa ndi ng’ombe n’kuzipereka kwa Abimeleki.+ Kenako awiriwo anachita pangano.+ Genesis 31:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Tiye tichite pangano+ ine ndi iwe, kuti likhale mboni pakati pa ine ndi iwe.”+
27 Ndiyeno Abulahamu anatenga nkhosa ndi ng’ombe n’kuzipereka kwa Abimeleki.+ Kenako awiriwo anachita pangano.+