Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 25:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Anyamatawa anakula, ndipo Esau anakhala munthu wodziwa kusaka,+ munthu wokonda kuyenda m’tchire. Koma Yakobo anali kukhala nthawi yambiri m’mahema.+ Iye anali munthu wosalakwa.+

  • Genesis 27:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Zitatero, Rabeka anatenga zovala zokongola koposa za mwana wake wamkulu Esau,+ zimene anali nazo m’nyumba.+ Zovalazo anaveka mwana wake wamng’ono, Yakobo.+

  • Nyimbo ya Solomo 4:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Milomo yako imangokhalira kukha uchi wapachisa,+ iwe mkwatibwi wanga. Uchi+ ndi mkaka zili kuseri kwa lilime lako, ndipo kununkhira kwa zovala zako kuli ngati kununkhira+ kwa nkhalango ya Lebanoni.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena