Genesis 31:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Pa zaka 20 zonsezi zimene ndakhala nanu, nkhosa zanu zazikazi ndi mbuzi zanu zazikazi sizinaberekepo mwana wakufa.+ Ndiponso, chikhalire sindinadyeko ndi imodzi yomwe ya nkhosa zanu zamphongo. Aefeso 6:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 pakuti mukudziwa kuti chabwino chilichonse chimene wina aliyense angachite adzachilandiranso kwa Yehova,+ kaya munthuyo akhale kapolo kapena mfulu.+
38 Pa zaka 20 zonsezi zimene ndakhala nanu, nkhosa zanu zazikazi ndi mbuzi zanu zazikazi sizinaberekepo mwana wakufa.+ Ndiponso, chikhalire sindinadyeko ndi imodzi yomwe ya nkhosa zanu zamphongo.
8 pakuti mukudziwa kuti chabwino chilichonse chimene wina aliyense angachite adzachilandiranso kwa Yehova,+ kaya munthuyo akhale kapolo kapena mfulu.+