Genesis 27:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mulungu woona akupatse mame akumwamba,+ ndi nthaka yachonde ya dziko lapansi.+ Achulukitsenso zokolola zako ndi vinyo wako watsopano.+ Deuteronomo 4:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 chifaniziro cha nyama iliyonse ya padziko lapansi,+ chifaniziro cha mbalame iliyonse youluka m’mlengalenga,+ 1 Mafumu 8:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 “Kumwamba kukatsekeka, mvula n’kumakanika kugwa+ chifukwa choti anali kukuchimwirani,+ ndiyeno iwo n’kupemphera atayang’ana malo ano,+ ndi kutamanda dzina lanu ndiponso kusiya tchimo lawo chifukwa choti mwakhala mukuwasautsa,+
28 Mulungu woona akupatse mame akumwamba,+ ndi nthaka yachonde ya dziko lapansi.+ Achulukitsenso zokolola zako ndi vinyo wako watsopano.+
17 chifaniziro cha nyama iliyonse ya padziko lapansi,+ chifaniziro cha mbalame iliyonse youluka m’mlengalenga,+
35 “Kumwamba kukatsekeka, mvula n’kumakanika kugwa+ chifukwa choti anali kukuchimwirani,+ ndiyeno iwo n’kupemphera atayang’ana malo ano,+ ndi kutamanda dzina lanu ndiponso kusiya tchimo lawo chifukwa choti mwakhala mukuwasautsa,+