Genesis 31:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Muluwu ndiponso mwala wachikumbutsowu ndi mboni.+ Zikuchitira umboni kuti, pakati pa ine ndi iwe, wina sadzadutsa muluwu ndi mwala wachikumbutsowu kukachitira mnzake choipa.+ Oweruza 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako nzika zonse za Sekemu ndi anthu onse m’nyumba ya Milo+ anasonkhana pamodzi kumene kunali chipilala pafupi ndi mtengo waukulu+ ku Sekemu.+ Kumeneko analonga Abimeleki ufumu.+
52 Muluwu ndiponso mwala wachikumbutsowu ndi mboni.+ Zikuchitira umboni kuti, pakati pa ine ndi iwe, wina sadzadutsa muluwu ndi mwala wachikumbutsowu kukachitira mnzake choipa.+
6 Kenako nzika zonse za Sekemu ndi anthu onse m’nyumba ya Milo+ anasonkhana pamodzi kumene kunali chipilala pafupi ndi mtengo waukulu+ ku Sekemu.+ Kumeneko analonga Abimeleki ufumu.+