Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 49:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Usakhale wopambana, chifukwa ndi khalidwe lako lotayirira ngati madzi osefukira,+ unakwera pogona bambo ako.+ Unaipitsa bedi langa pa nthawiyo.+ Anagonapo ndithu ameneyu!

  • Levitiko 18:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 “‘Usavule mkazi wa bambo ako,+ chifukwa kumeneko n’kuvula bambo ako.

  • 1 Mbiri 5:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Mwana woyamba wa Isiraeli anali Rubeni.+ Iye anali woyamba kubadwa+ koma chifukwa chakuti anaipitsa bedi la bambo wake,+ udindo wake monga woyamba kubadwa unaperekedwa kwa ana a Yosefe,+ mwana wa Isiraeli. Choncho iye sanalembedwe monga woyamba kubadwa pamndandanda wa mayina wotsatira makolo.

  • 1 Akorinto 5:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Mbiri yamvekatu kuti pakuchitika dama*+ pakati panu, ndipo dama lake ndi loti ngakhale anthu a mitundu ina sachita. Akuti mwamuna wina watengana ndi mkazi wa bambo ake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena