Genesis 25:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Isaki anali ndi zaka 40 pamene anakwatira Rabeka, mwana wa Betuele,+ Msiriya+ wa ku Padana-ramu, mlongo wake wa Labani, Msiriya. Genesis 25:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pambuyo pa iyeyu, panabadwa m’bale wake, dzanja lake litagwira chidendene cha Esau,+ choncho Isaki anapatsa mwanayo dzina lakuti Yakobo.+ Pamene Rabeka amabereka anawa n’kuti Isaki ali ndi zaka 60.
20 Isaki anali ndi zaka 40 pamene anakwatira Rabeka, mwana wa Betuele,+ Msiriya+ wa ku Padana-ramu, mlongo wake wa Labani, Msiriya.
26 Pambuyo pa iyeyu, panabadwa m’bale wake, dzanja lake litagwira chidendene cha Esau,+ choncho Isaki anapatsa mwanayo dzina lakuti Yakobo.+ Pamene Rabeka amabereka anawa n’kuti Isaki ali ndi zaka 60.