Genesis 25:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 M’kupita kwa nthawi, mkaziyo anamuberekera Zimirani, Yokesani, Medani, Midiyani,+ Isibaki ndi Shuwa.+ Ekisodo 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Patapita nthawi, Farao anaimva nkhaniyi ndipo anafuna kupha Mose.+ Koma Mose anam’thawa+ Farao ndipo anapita kukakhala kudziko la Midiyani.+ Atafika kumeneko, anakhala pachitsime. Numeri 31:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Uwabwezere+ Amidiyani+ pa zimene anachitira ana a Isiraeli. Pambuyo pake udzaikidwa m’manda kuti ukagone ndi makolo ako.”+
2 M’kupita kwa nthawi, mkaziyo anamuberekera Zimirani, Yokesani, Medani, Midiyani,+ Isibaki ndi Shuwa.+
15 Patapita nthawi, Farao anaimva nkhaniyi ndipo anafuna kupha Mose.+ Koma Mose anam’thawa+ Farao ndipo anapita kukakhala kudziko la Midiyani.+ Atafika kumeneko, anakhala pachitsime.
2 “Uwabwezere+ Amidiyani+ pa zimene anachitira ana a Isiraeli. Pambuyo pake udzaikidwa m’manda kuti ukagone ndi makolo ako.”+