Genesis 31:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Nyama yanu iliyonse imene inakhadzulidwa ndi chilombo sindinaibweretse kwa inu.+ Ndinali kuitenga kukhala yanga. Kaya ina ibedwe usana kapena usiku, munali kundiuza kuti ndikulipireni.+ Ekisodo 22:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ngati nyamayo inaphedwa ndi chilombo,+ azibweretsa nyama yakufayo monga umboni.+ Asalipire pa nyama iliyonse yophedwa ndi chilombo.
39 Nyama yanu iliyonse imene inakhadzulidwa ndi chilombo sindinaibweretse kwa inu.+ Ndinali kuitenga kukhala yanga. Kaya ina ibedwe usana kapena usiku, munali kundiuza kuti ndikulipireni.+
13 Ngati nyamayo inaphedwa ndi chilombo,+ azibweretsa nyama yakufayo monga umboni.+ Asalipire pa nyama iliyonse yophedwa ndi chilombo.