Genesis 39:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pamenepo, mbuye wake wa Yosefe anatenga Yosefeyo n’kumupereka kundende ya akaidi a mfumu, ndipo anakhala kumeneko.+ Salimo 105:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kumeneko anasautsa mapazi ake ndi matangadza,+Anam’manga ndi maunyolo.+
20 Pamenepo, mbuye wake wa Yosefe anatenga Yosefeyo n’kumupereka kundende ya akaidi a mfumu, ndipo anakhala kumeneko.+