Genesis 40:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Usiku wina,+ woperekera chikho ndi wophika mkate, atumiki a mfumu ya Iguputo omwe anali m’ndende+ aja, analota maloto.+ Aliyense analota maloto ake okhala ndi tanthauzo lakelake.+
5 Usiku wina,+ woperekera chikho ndi wophika mkate, atumiki a mfumu ya Iguputo omwe anali m’ndende+ aja, analota maloto.+ Aliyense analota maloto ake okhala ndi tanthauzo lakelake.+