1 Mafumu 11:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Yerobowamu anali mwamuna wamphamvu ndi wolimba mtima.+ Solomo ataona kuti mnyamatayo anali wogwira ntchito molimbika,+ anamuika kukhala woyang’anira+ ntchito yonse yokakamiza+ ya kunyumba ya Yosefe.+
28 Yerobowamu anali mwamuna wamphamvu ndi wolimba mtima.+ Solomo ataona kuti mnyamatayo anali wogwira ntchito molimbika,+ anamuika kukhala woyang’anira+ ntchito yonse yokakamiza+ ya kunyumba ya Yosefe.+