Genesis 42:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Anapitiriza kuti: “Ine ndamva kuti ku Iguputo kuli tirigu.+ Pitani kumeneko mukatigulire tirigu kuti tikhalebe ndi moyo, tingafe ndi njala.” Maliro 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Amene anaphedwa ndi lupanga+ aliko bwino kusiyana ndi amene anafa ndi njala,+Pakuti amene anafa ndi njala anafooka chifukwa chosowa chakudya, ndipo anakhala ngati apyozedwa ndi lupanga.
2 Anapitiriza kuti: “Ine ndamva kuti ku Iguputo kuli tirigu.+ Pitani kumeneko mukatigulire tirigu kuti tikhalebe ndi moyo, tingafe ndi njala.”
9 Amene anaphedwa ndi lupanga+ aliko bwino kusiyana ndi amene anafa ndi njala,+Pakuti amene anafa ndi njala anafooka chifukwa chosowa chakudya, ndipo anakhala ngati apyozedwa ndi lupanga.