Genesis 37:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndinalota tikumanga mitolo ya tirigu pakati pa munda. Mtolo wanga unadzuka n’kuima chilili. Mitolo yanunso inadzuka, ndipo inazungulira mtolo wanga n’kuyamba kuuweramira.”+ Genesis 50:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako abale akewonso anafika, n’kudzigwetsa pansi pamaso pake, n’kunena kuti: “Tikudzipereka kwa inu ngati akapolo anu.”+
7 Ndinalota tikumanga mitolo ya tirigu pakati pa munda. Mtolo wanga unadzuka n’kuima chilili. Mitolo yanunso inadzuka, ndipo inazungulira mtolo wanga n’kuyamba kuuweramira.”+
18 Kenako abale akewonso anafika, n’kudzigwetsa pansi pamaso pake, n’kunena kuti: “Tikudzipereka kwa inu ngati akapolo anu.”+