Genesis 44:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 N’chifukwa chiyani mwaba kapu yomwera mbuye wanga, imenenso amaombezera pofuna kudziwa zinthu?+ Mwachita chinthu choipa kwambiri.’”
5 N’chifukwa chiyani mwaba kapu yomwera mbuye wanga, imenenso amaombezera pofuna kudziwa zinthu?+ Mwachita chinthu choipa kwambiri.’”