Genesis 42:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pa tsiku lachitatu, Yosefe anawauza kuti: “Popeza ine ndimaopa+ Mulungu woona, chitani izi kuti mukhale ndi moyo:
18 Pa tsiku lachitatu, Yosefe anawauza kuti: “Popeza ine ndimaopa+ Mulungu woona, chitani izi kuti mukhale ndi moyo: