Genesis 44:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Amene apezeke ndi kapuyo mwa akapolo anufe aphedwe, ndipo enafe tikhale akapolo anu mbuyathu.”+