Genesis 26:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Tilumbirirane kuti sudzatichitira choipa chilichonse, pakuti ifenso sitinakukhudze. Tinakuchitira zabwino zokhazokha, mwa kukuchotsa kwathu mwamtendere.+ Tsopano Yehova wakudalitsa.’”+
29 Tilumbirirane kuti sudzatichitira choipa chilichonse, pakuti ifenso sitinakukhudze. Tinakuchitira zabwino zokhazokha, mwa kukuchotsa kwathu mwamtendere.+ Tsopano Yehova wakudalitsa.’”+