Genesis 35:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pomalizira pake, pamene moyo wake+ unali kutayika (pakuti anamwalira),+ anatcha mwanayo dzina lakuti Beni-oni.* Koma bambo ake anamutcha Benjamini.*+ Genesis 37:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Bambo awo anauyang’anitsitsa mkanjowo. Ndiyeno anafuula kuti: “Kalanga ine! Mkanjowu ndi wa mwana wanga! Chilombo cholusa chamudya basi mwana wanga.+ Wakhadzulidwa+ ndithu mwana wanga Yosefe!”
18 Pomalizira pake, pamene moyo wake+ unali kutayika (pakuti anamwalira),+ anatcha mwanayo dzina lakuti Beni-oni.* Koma bambo ake anamutcha Benjamini.*+
33 Bambo awo anauyang’anitsitsa mkanjowo. Ndiyeno anafuula kuti: “Kalanga ine! Mkanjowu ndi wa mwana wanga! Chilombo cholusa chamudya basi mwana wanga.+ Wakhadzulidwa+ ndithu mwana wanga Yosefe!”