Genesis 42:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndiyeno mukabweretse mng’ono wanuyo kwa ine. Mukatero, ndidzatsimikiza kuti mukunena zoona, ndipo simudzaphedwa.”+ Iwo anavomereza kuchita zimenezo. Genesis 43:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma Yuda anauza bambo ake kuti:+ “Munthu ujatu anatichenjeza mwamphamvu kuti, ‘Musadzayese n’komwe kuonekeranso pamaso panga mukadzalephera kubwera naye m’bale wanuyo.’+
20 Ndiyeno mukabweretse mng’ono wanuyo kwa ine. Mukatero, ndidzatsimikiza kuti mukunena zoona, ndipo simudzaphedwa.”+ Iwo anavomereza kuchita zimenezo.
3 Koma Yuda anauza bambo ake kuti:+ “Munthu ujatu anatichenjeza mwamphamvu kuti, ‘Musadzayese n’komwe kuonekeranso pamaso panga mukadzalephera kubwera naye m’bale wanuyo.’+