Genesis 50:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Pamenepo Yosefe anakumbatira mtembo wa bambo ake+ ndipo analira kwambiri n’kuupsompsona.+