Ekisodo 6:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndipo ana aamuna a Simiyoni anali Yemueli, Yamini, Ohadi, Yakini, Zohari ndi Shauli, mwana amene anabereka ndi mkazi wachikanani.+ Amenewa ndiwo mabanja a fuko la Simiyoni.+ 1 Mbiri 4:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ana a Simiyoni anali Nemueli,+ Yamini,+ Yaribi, Zera, ndi Shauli.+
15 Ndipo ana aamuna a Simiyoni anali Yemueli, Yamini, Ohadi, Yakini, Zohari ndi Shauli, mwana amene anabereka ndi mkazi wachikanani.+ Amenewa ndiwo mabanja a fuko la Simiyoni.+